Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 138:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ngakhale nditakumana ndi mavuto, inu mudzandithandiza kuti ndikhalebe ndi moyo.+

      Mumagwiritsa ntchito mphamvu zanu polimbana ndi adani anga omwe ndi okwiya.

      Dzanja lanu lamanja lidzandipulumutsa.

  • Yesaya 43:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ukamadzadutsa pamadzi, ine ndidzakhala nawe.+

      Ukamadzawoloka mitsinje, madzi sadzakukokolola.+

      Ukamadzayenda pamoto sudzapsa

      Ndipo ngakhale lawi la moto silidzakuwaula.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena