Salimo 71:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngakhale nditakalamba nʼkumera imvi, inu Mulungu musandisiye.+ Ndiloleni kuti ndiuze mʼbadwo wotsatira za mphamvu zanu*Komanso za nyonga zanu kwa onse obwera mʼtsogolo.+ Miyambo 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Imvi ndi chisoti chachifumu cha ulemerero+Zikapezeka ndi munthu amene akuyenda mʼnjira yachilungamo.+ Yesaya 40:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma anthu amene amayembekezera Yehova adzapezanso mphamvu. Iwo adzaulukira mʼmwamba ngati kuti ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka.Adzayenda koma osatopa.”+ Yesaya 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale mudzakalambe, ine ndidzakhala chimodzimodzi.+Ngakhale tsitsi lanu lidzachite imvi, ine ndidzapitiriza kukunyamulani. Ndidzakunyamulani, kukuthandizani komanso kukupulumutsani ngati mmene ndakhala ndikuchitira.+
18 Ngakhale nditakalamba nʼkumera imvi, inu Mulungu musandisiye.+ Ndiloleni kuti ndiuze mʼbadwo wotsatira za mphamvu zanu*Komanso za nyonga zanu kwa onse obwera mʼtsogolo.+
31 Imvi ndi chisoti chachifumu cha ulemerero+Zikapezeka ndi munthu amene akuyenda mʼnjira yachilungamo.+
31 Koma anthu amene amayembekezera Yehova adzapezanso mphamvu. Iwo adzaulukira mʼmwamba ngati kuti ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka.Adzayenda koma osatopa.”+
4 Ngakhale mudzakalambe, ine ndidzakhala chimodzimodzi.+Ngakhale tsitsi lanu lidzachite imvi, ine ndidzapitiriza kukunyamulani. Ndidzakunyamulani, kukuthandizani komanso kukupulumutsani ngati mmene ndakhala ndikuchitira.+