Salimo 119:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Ine ndine mnzawo wa anthu amene amakuopani,Ndiponso wa anthu amene amasunga malamulo anu.+