Deuteronomo 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu nʼkutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchenjezani lero kuti anthu inu mudzatha ndithu.+ Salimo 97:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Onse amene akutumikira chifaniziro chilichonse achite manyazi,+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yawo yopanda pake.+ Muweramireni,* inu milungu yonse.+ Yona 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu okhulupirira mafano opanda pake, amasiya Mulungu amene angawasonyeze chikondi chokhulupirika.*
19 Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu nʼkutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchenjezani lero kuti anthu inu mudzatha ndithu.+
7 Onse amene akutumikira chifaniziro chilichonse achite manyazi,+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yawo yopanda pake.+ Muweramireni,* inu milungu yonse.+
8 Anthu okhulupirira mafano opanda pake, amasiya Mulungu amene angawasonyeze chikondi chokhulupirika.*