Yesaya 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzakwezeka chifukwa cha chiweruzo chake.*Mulungu woona, Woyera,+ adzadziyeretsa kudzera mʼchilungamo.+
16 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzakwezeka chifukwa cha chiweruzo chake.*Mulungu woona, Woyera,+ adzadziyeretsa kudzera mʼchilungamo.+