Salimo 93:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 93 Yehova wakhala Mfumu!+ Iye wavala ulemerero.Yehova wavala mphamvuWazivala ngati lamba wamʼchiuno. Dziko lapansi lakhazikika,Moti silingasunthidwe.* Chivumbulutso 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo ankanena kuti: “Tikukuthokozani inu Yehova,* Mulungu Wamphamvuyonse, inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu zanu zazikulu nʼkuyamba kulamulira monga mfumu.+
93 Yehova wakhala Mfumu!+ Iye wavala ulemerero.Yehova wavala mphamvuWazivala ngati lamba wamʼchiuno. Dziko lapansi lakhazikika,Moti silingasunthidwe.*
17 Iwo ankanena kuti: “Tikukuthokozani inu Yehova,* Mulungu Wamphamvuyonse, inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu zanu zazikulu nʼkuyamba kulamulira monga mfumu.+