Levitiko 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza gulu lonse la Aisiraeli kuti, ‘Mukhale oyera, chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+