1 Samueli 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Samueli anatenga mwana wa nkhosa woyamwa nʼkumupereka nsembe yopsereza+ yathunthu kwa Yehova. Atatero anapemphera kwa Yehova kuti athandize Aisiraeli ndipo Yehova anamuyankha.+
9 Ndiyeno Samueli anatenga mwana wa nkhosa woyamwa nʼkumupereka nsembe yopsereza+ yathunthu kwa Yehova. Atatero anapemphera kwa Yehova kuti athandize Aisiraeli ndipo Yehova anamuyankha.+