-
Ekisodo 15:24, 25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Choncho anthu anayamba kungʼungʼudza motsutsana ndi Mose+ kuti: “Timwa chiyani?” 25 Zitatero Mose anafuulira Yehova+ ndipo Yehova anamusonyeza kamtengo. Mose anaponya kamtengoko mʼmadzi moti madziwo anakhala okoma.
Pamalo amenewo Mulungu anawapatsa lamulo ndi maziko operekera chiweruzo, ndipo kumeneko anawayesa.+
-
-
1 Samueli 15:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndiyeno Yehova anauza Samueli kuti:
-