Salimo 95:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 95 Bwerani, tiyeni tifuule kwa Yehova mosangalala! Tiyeni tifuule mosangalala ndipo titamande Thanthwe la chipulumutso chathu.+ 2 Tiyeni tikaonekere pamaso pake moyamikira.+Tiyeni timuimbire nyimbo zomutamanda ndipo tifuule mosangalala. Salimo 98:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Dziko lonse lapansi lifuulire Yehova mosangalala chifukwa wapambana. Kondwerani ndipo fuulani mosangalala komanso imbani nyimbo zomutamanda.+
95 Bwerani, tiyeni tifuule kwa Yehova mosangalala! Tiyeni tifuule mosangalala ndipo titamande Thanthwe la chipulumutso chathu.+ 2 Tiyeni tikaonekere pamaso pake moyamikira.+Tiyeni timuimbire nyimbo zomutamanda ndipo tifuule mosangalala.
4 Dziko lonse lapansi lifuulire Yehova mosangalala chifukwa wapambana. Kondwerani ndipo fuulani mosangalala komanso imbani nyimbo zomutamanda.+