Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iweyo ukayenda mʼnjira zanga ngati mmene bambo ako Davide anachitira,+ yemwe anali ndi mtima wokhulupirika+ komanso ankachita zoyenera,+ ukachita zonse zimene ndinakulamula,+ ndiponso ukamamvera malangizo anga ndi ziweruzo zanga,+

  • Salimo 78:70
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 70 Anasankha Davide+ mtumiki wake,

      Ndipo anamuchotsa kumakola a nkhosa,+

  • Salimo 78:72
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 72 Iye anawaweta ndi mtima wokhulupirika,+

      Ndipo anawatsogolera mwaluso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena