Salimo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwafufuza mtima wanga, mwandifufuza ngakhale usiku,+Ndipo mwandiyenga.+Mudzapeza kuti ndinalibe zolinga zochita choipa chilichonse.Ndipo pakamwa panga sipanachimwe. Salimo 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndifufuzeni, inu Yehova, ndipo mundiyese.Yengani maganizo anga* komanso mtima wanga.+
3 Mwafufuza mtima wanga, mwandifufuza ngakhale usiku,+Ndipo mwandiyenga.+Mudzapeza kuti ndinalibe zolinga zochita choipa chilichonse.Ndipo pakamwa panga sipanachimwe.