Salimo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndafooka chifukwa cha kuusa moyo kwanga.+Usiku wonse ndimanyowetsa bedi langa* ndi misozi,Ndimalira ndipo misozi imadzaza pabedi panga.+ Salimo 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Thupi langa lonse lachita dzanzi ndipo ndilibiretu mphamvu.Ndikubuula mokweza* chifukwa cha kuvutika kwa mtima wanga.
6 Ndafooka chifukwa cha kuusa moyo kwanga.+Usiku wonse ndimanyowetsa bedi langa* ndi misozi,Ndimalira ndipo misozi imadzaza pabedi panga.+
8 Thupi langa lonse lachita dzanzi ndipo ndilibiretu mphamvu.Ndikubuula mokweza* chifukwa cha kuvutika kwa mtima wanga.