Salimo 78:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sitidzazibisa kwa ana awo.Tidzafotokozera mʼbadwo wamʼtsogolo+Tidzawafotokozera zinthu zotamandika zimene Yehova anachita komanso mphamvu zake,+Zinthu zodabwitsa zimene wachita.+ Aroma 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa nʼcholinga choti tikhale ndi chiyembekezo.+
4 Sitidzazibisa kwa ana awo.Tidzafotokozera mʼbadwo wamʼtsogolo+Tidzawafotokozera zinthu zotamandika zimene Yehova anachita komanso mphamvu zake,+Zinthu zodabwitsa zimene wachita.+
4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa nʼcholinga choti tikhale ndi chiyembekezo.+