Yobu 36:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Inde Mulungu ndi wamkulu kuposa mmene tikudziwira.+Palibe amene angawerenge* zaka zimene wakhala ndi moyo.+ Malaki 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ine ndine Yehova ndipo sindisintha.*+ Inu ndinu ana a Yakobo ndipo simunatheretu. Yakobo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba.+ Imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zakuthambo,+ amene sasintha ngati mthunzi umene umasunthasuntha.+
26 Inde Mulungu ndi wamkulu kuposa mmene tikudziwira.+Palibe amene angawerenge* zaka zimene wakhala ndi moyo.+
17 Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba.+ Imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zakuthambo,+ amene sasintha ngati mthunzi umene umasunthasuntha.+