Salimo 56:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa inu mwandipulumutsa* ku imfa.+Ndipo mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyende pamaso pa Mulungu mʼkuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+
13 Chifukwa inu mwandipulumutsa* ku imfa.+Ndipo mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyende pamaso pa Mulungu mʼkuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+