Salimo 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mumandipatsa chakudya patebulo pamaso pa adani anga.+ Ndimatsitsimulidwa mukandidzoza mafuta kumutu.+Kapu yanga ndi yodzaza bwino.+ Salimo 65:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wosangalala ndi munthu amene inu mwamusankha nʼkumubweretsa pafupi ndi inu,Kuti akhale mʼmabwalo anu.+ Tidzakhutira ndi zinthu zabwino zamʼnyumba yanu,+Kachisi wanu woyera.*+
5 Mumandipatsa chakudya patebulo pamaso pa adani anga.+ Ndimatsitsimulidwa mukandidzoza mafuta kumutu.+Kapu yanga ndi yodzaza bwino.+
4 Wosangalala ndi munthu amene inu mwamusankha nʼkumubweretsa pafupi ndi inu,Kuti akhale mʼmabwalo anu.+ Tidzakhutira ndi zinthu zabwino zamʼnyumba yanu,+Kachisi wanu woyera.*+