Salimo 51:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Bwezeretsani mwa ine chisangalalo chimene chimabwera chifukwa cha chipulumutso chanu.+Ndipatseni mtima wofunitsitsa kukumverani.* Yesaya 40:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma anthu amene amayembekezera Yehova adzapezanso mphamvu. Iwo adzaulukira mʼmwamba ngati kuti ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka.Adzayenda koma osatopa.”+
12 Bwezeretsani mwa ine chisangalalo chimene chimabwera chifukwa cha chipulumutso chanu.+Ndipatseni mtima wofunitsitsa kukumverani.*
31 Koma anthu amene amayembekezera Yehova adzapezanso mphamvu. Iwo adzaulukira mʼmwamba ngati kuti ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka.Adzayenda koma osatopa.”+