Salimo 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwaipatsa madalitso mpaka kalekale.+Mwaichititsa kuti ikhale yosangalala chifukwa muli nayo pafupi.*+ Mateyu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Osangalala ndi anthu oyera mtima+ chifukwa adzaona Mulungu.
6 Mwaipatsa madalitso mpaka kalekale.+Mwaichititsa kuti ikhale yosangalala chifukwa muli nayo pafupi.*+