Yakobo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba.+ Imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zakuthambo,+ amene sasintha ngati mthunzi umene umasunthasuntha.+ 1 Yohane 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ife tamva uthenga kuchokera kwa iye ndipo tikuulengeza kwa inu. Uthenga wake ndi wakuti, Mulungu ndiye kuwala+ ndipo kwa iye kulibe mdima ngakhale pangʼono.
17 Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba.+ Imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zakuthambo,+ amene sasintha ngati mthunzi umene umasunthasuntha.+
5 Ife tamva uthenga kuchokera kwa iye ndipo tikuulengeza kwa inu. Uthenga wake ndi wakuti, Mulungu ndiye kuwala+ ndipo kwa iye kulibe mdima ngakhale pangʼono.