Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 38:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Kodi unali kuti pamene ndinkaika maziko a dziko lapansi?+

      Ndiuze ngati ukudziwa mmene zinakhalira.

  • Yobu 38:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Kodi zipilala zake zinazikidwa pachiyani?

      Kapena ndi ndani amene anaika mwala wake wapakona,+

  • Salimo 24:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Dziko lapansi ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndi za Yehova,+

      Nthaka komanso onse okhala panthakapo ndi ake.

       2 Iye anakhazika dziko lapansi molimba panyanja+

      Ndipo analikhazikitsa mwamphamvu pamitsinje.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena