Mlaliki 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chakudya chimachititsa kuti anthu aziseka, ndipo vinyo amachititsa kuti moyo ukhale wosangalatsa,+ koma ndalama zimathandiza munthu kupeza chilichonse chimene akufuna.+
19 Chakudya chimachititsa kuti anthu aziseka, ndipo vinyo amachititsa kuti moyo ukhale wosangalatsa,+ koma ndalama zimathandiza munthu kupeza chilichonse chimene akufuna.+