Salimo 78:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Iye anathamangitsa mitundu ya anthu kuichotsa pamaso pawo.+Iye anawagawira dzikolo kuti likhale cholowa chawo pochita kuwayezera ndi chingwe.+Anachititsa mafuko a Isiraeli kuti akhale mʼnyumba zawozawo.+
55 Iye anathamangitsa mitundu ya anthu kuichotsa pamaso pawo.+Iye anawagawira dzikolo kuti likhale cholowa chawo pochita kuwayezera ndi chingwe.+Anachititsa mafuko a Isiraeli kuti akhale mʼnyumba zawozawo.+