Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 26:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Nthawi yomweyo Abimeleki anaitanitsa Isaki nʼkumufunsa kuti: “Ameneyu ndi mkazi wako eti? Nanga nʼchifukwa chiyani unanena kuti, ‘Ndi mchemwali wangaʼ?” Ndiyeno Isaki anayankha kuti: “Ndinanena choncho poopa kuti andipha chifukwa cha iye.”+

  • Genesis 26:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako Abimeleki analamula anthu ake onse kuti: “Aliyense amene angavutitse munthu uyu komanso mkazi wake, aphedwa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena