2 Samueli 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso pamene Abisalomu ankapereka nsembe, anaitanitsa Ahitofeli+ wa ku Gilo, mlangizi wa Davide,+ kuchoka kumzinda wakwawo wa Gilo.+ Anthu amene anagwirizana ndi Abisalomu pa chiwembuchi anapitiriza kuwonjezeka.+ 2 Samueli 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Abisalomu ndi amuna onse a Isiraeli, anafika ku Yerusalemu ndipo Ahitofeli+ anali naye limodzi.
12 Komanso pamene Abisalomu ankapereka nsembe, anaitanitsa Ahitofeli+ wa ku Gilo, mlangizi wa Davide,+ kuchoka kumzinda wakwawo wa Gilo.+ Anthu amene anagwirizana ndi Abisalomu pa chiwembuchi anapitiriza kuwonjezeka.+