-
Genesis 41:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Choncho inu Farao mufufuze munthu wozindikira ndi wanzeru, ndipo mumuike kuti akhale woyangʼanira dziko la Iguputo.
-
-
Genesis 41:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Ndiyeno Farao anafunsa antchito ake kuti: “Kodi pangapezekenso munthu wina ngati uyu, amene ali ndi mzimu wa Mulungu?”
-