-
Machitidwe 7:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Nthawi itayandikira, yoti lonjezo limene Mulungu anapereka kwa Abulahamu likwaniritsidwe, mbadwa za Yakobo zinachuluka kwambiri ku Iguputo.
-