Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tiyeni tiwachenjerere anthu amenewa kuti asapitirize kuchulukana, kuopera kuti pa nthawi ya nkhondo angadzagwirizane ndi adani athu nʼkumenyana nafe kenako nʼkuchoka mʼdziko muno.”

  • Machitidwe 7:18, 19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kenako, mfumu ina yomwe sinkadziwa za Yosefe inayamba kulamulira ku Iguputo.+ 19 Mfumu imeneyi inachenjerera anthu a mtundu wathu komanso inakakamiza makolo athuwo kuti azitaya makanda awo nʼcholinga choti asakhale ndi moyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena