Ekisodo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zitatero, Yehova anakwiyira kwambiri Mose ndipo anati: “Kodi si paja Aroni+ Mlevi uja ndi mʼbale wako? Ndikudziwa kuti amalankhula bwino kwambiri. Ndiponso, iye ali mʼnjira kudzakuchingamira. Akakuona, adzakondwera kwambiri mumtima mwake.+ Ekisodo 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Taona, ndakuika kuti ukhale ngati Mulungu* kwa Farao, ndipo Aroni mchimwene wako akhala mneneri wako.+
14 Zitatero, Yehova anakwiyira kwambiri Mose ndipo anati: “Kodi si paja Aroni+ Mlevi uja ndi mʼbale wako? Ndikudziwa kuti amalankhula bwino kwambiri. Ndiponso, iye ali mʼnjira kudzakuchingamira. Akakuona, adzakondwera kwambiri mumtima mwake.+
7 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Taona, ndakuika kuti ukhale ngati Mulungu* kwa Farao, ndipo Aroni mchimwene wako akhala mneneri wako.+