-
Ekisodo 8:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho Aroni anatambasula dzanja lake nʼkuloza madzi onse a mu Iguputo, ndipo achule anayamba kutuluka ndi kudzaza dziko lonse la Iguputo.
-