Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu nʼkumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbadwa* zako.”+ Choncho Abulamu anamanga guwa lansembe pamalo amene Yehova anaonekera kwa iye.

  • Genesis 15:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno Mulungu anauza Abulamu kuti: “Udziwe ndithu kuti mbadwa* zako zidzakhala alendo mʼdziko la eni ndipo anthu adzazisandutsa akapolo ndi kuzizunza kwa zaka 400.+ 14 Koma mtundu umene adzautumikirewo ndidzauweruza.+ Pambuyo pake, iwo adzachokako ndi katundu wambiri.+

  • Ekisodo 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Patapita nthawi, Mulungu anamva kubuula+ kwawo ndipo anakumbukira pangano lake ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo.+

  • Deuteronomo 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Sikuti mukulowa mʼdzikoli kukalitenga kukhala lanu chifukwa choti ndinu olungama kapena chifukwa choti ndinu owongoka mtima. Koma Yehova Mulungu wanu akuthamangitsira mitundu imeneyi kutali ndi inu,+ chifukwa choti ndi yoipa, ndiponso kuti Yehova akwaniritse mawu onse amene analumbirira makolo anu Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena