Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 16:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Yamikani Yehova chifukwa iye ndi wabwino,+

      Chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.+

  • Ezara 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iwo anayamba kuimba+ potamanda ndi kuyamika Yehova kuti, “iye ndi wabwino, chikondi chokhulupirika chimene amachisonyeza kwa Isiraeli chidzakhalapo mpaka kalekale.”+ Kenako anthu onse anafuula kwambiri potamanda Yehova chifukwa cha kumangidwa kwa maziko a nyumba ya Yehova.

  • Salimo 103:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma Yehova adzapitiriza kusonyeza chikondi chake chokhulupirika mpaka kalekale

      Kwa anthu amene amamuopa,+

      Ndipo adzapitiriza kusonyeza chilungamo chake kwa ana a ana awo.+

  • Salimo 107:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 107 Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+

      Chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapobe mpaka kalekale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena