Ezara 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinanena kuti: “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi kuti ndikweze nkhope yanga kuyangʼana kwa inu Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu zachuluka kupitirira pamutu pathu ndipo machimo athu aunjikana mpaka kumwamba.+ Danieli 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ife tachimwa, tachita zinthu zolakwika komanso zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka nʼkusiya kutsatira malamulo ndi zigamulo zanu.
6 Kenako ndinanena kuti: “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi kuti ndikweze nkhope yanga kuyangʼana kwa inu Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu zachuluka kupitirira pamutu pathu ndipo machimo athu aunjikana mpaka kumwamba.+
5 Ife tachimwa, tachita zinthu zolakwika komanso zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka nʼkusiya kutsatira malamulo ndi zigamulo zanu.