Ekisodo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawiyo Mose ndi Aisiraeli anaimbira Yehova nyimbo iyi:+ “Ndiimbira Yehova, chifukwa walemekezeka kwambiri.+ Mahatchi ndi okwera pamahatchiwo wawaponyera mʼnyanja.+
15 Pa nthawiyo Mose ndi Aisiraeli anaimbira Yehova nyimbo iyi:+ “Ndiimbira Yehova, chifukwa walemekezeka kwambiri.+ Mahatchi ndi okwera pamahatchiwo wawaponyera mʼnyanja.+