Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ngati akupereka nsembeyo posonyeza kuyamikira,+ azipereka nsembe yoyamikira pamodzi ndi mkate wozungulira woboola pakati, wopanda zofufumitsa, wothira mafuta. Aziperekanso timitanda ta mkate topyapyala topanda zofufumitsa, topaka mafuta komanso mkate wozungulira woboola pakati, wothira mafuta, wophika ndi ufa wosalala wosakaniza bwino ndi mafuta.

  • Salimo 50:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yamikani Mulungu kuti ikhale ngati nsembe imene mukupereka kwa iye,+

      Ndipo perekani kwa Wamʼmwambamwamba zimene mwalonjeza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena