-
Yona 1:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndiyeno Yehova anabweretsa mphepo yamphamvu panyanja, ndipo kenako panachitika chimkuntho choopsa, moti chombocho chinatsala pangʼono kusweka.
-
-
Yona 1:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma anthuwo anayesetsa kuti adutse mafunde amphamvuwo nʼkukafika kumtunda. Komabe sanakwanitse chifukwa mkunthowo unkawonjezeka kwambiri.
-