-
Yona 1:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kenako anthuwo anafuulira Yehova kuti: “Chonde Yehova, musalole kuti tife chifukwa cha munthu uyu! Musatiimbe mlandu wa magazi a munthu wosalakwa, chifukwa inu Yehova mwachita zimene mumafuna.”
-