Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 65:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Mumachititsa kuti nyanja imene ikuchita mafunde ikhale bata.+

      Mumaletsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+

  • Salimo 89:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Nyanja ikadzaza mumailamulira.+

      Mafunde ake akawinduka, inuyo mumawachititsa kuti akhale bata.+

  • Yona 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako ananyamula Yona nʼkumuponya mʼnyanja ndipo nyanjayo inakhala bata.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena