Salimo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,Mwachititsa kuti ulemerero wanu ukhale pamwamba kuposa kumwamba!+ Salimo 57:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Mulungu, kwezekani kupitirira kumwamba.Ulemerero wanu ukhale padziko lonse lapansi.+ Salimo 57:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Mulungu, kwezekani kupitirira kumwamba.Ulemerero wanu ukhale padziko lonse lapansi.+
8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,Mwachititsa kuti ulemerero wanu ukhale pamwamba kuposa kumwamba!+