Yoswa 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mose mtumiki wa Yehova anapereka cholowa kwa hafu ina ya fuko la Manase, kwa fuko la Rubeni ndi kwa fuko la Gadi, kutsidya lakumʼmawa kwa mtsinje wa Yorodano.+ Yoswa 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anapatsidwanso Giliyadi, dera la Agesuri, la Amaakati,+ phiri lonse la Herimoni ndi dera lonse la Basana+ mpaka ku Saleka.+
8 Mose mtumiki wa Yehova anapereka cholowa kwa hafu ina ya fuko la Manase, kwa fuko la Rubeni ndi kwa fuko la Gadi, kutsidya lakumʼmawa kwa mtsinje wa Yorodano.+
11 Anapatsidwanso Giliyadi, dera la Agesuri, la Amaakati,+ phiri lonse la Herimoni ndi dera lonse la Basana+ mpaka ku Saleka.+