-
Deuteronomo 33:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ulemerero wake ndi wofanana ndi wa mwana wa ngʼombe wamphongo woyamba kubadwa,
Ndipo nyanga zake ndi nyanga za ngʼombe yamphongo yamʼtchire.
Nyanga zimenezo adzakankha* nazo anthu.
Adzakankha nazo anthu onse pamodzi mpaka kukafika kumalekezero a dziko lapansi.
Nyanga zimenezo ndi anthu masauzande makumimakumi a fuko la Efuraimu,+
Ndiponso anthu masauzande a fuko la Manase.”
-