-
2 Samueli 15:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Abisalomu ankadzuka mʼmawa kwambiri nʼkukaima mʼmbali mwa msewu wopita kugeti la mzinda.+ Ndiyeno munthu aliyense akafika ndi mlandu woti uweruzidwe ndi mfumu,+ Abisalomu ankamuitana nʼkumufunsa kuti: “Wachokera mzinda uti?” Munthuyo ankamuuza fuko la Isiraeli limene wachokera. 3 Kenako Abisalomu ankamuuza kuti: “Zimene ukunenazi ndi zoona komanso zomveka. Koma kwa mfumu kulibe aliyense woti amvetsere nkhani yakoyi.”
-