Salimo 68:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+ Imbirani Iye amene akudutsa mʼchipululu.* Dzina lake ndi Ya.*+ Sangalalani pamaso pake. Salimo 113:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 113 Tamandani Ya!* Inu atumiki a Yehova, mutamandeni,Tamandani dzina la Yehova. Chivumbulutso 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu kumwamba amene ankamveka ngati mawu ofuula a khamu lalikulu akuti: “Tamandani Ya!*+ Mulungu wathu amapulumutsa anthu ndipo ali ndi mphamvu zazikulu komanso ulemerero,
4 Imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+ Imbirani Iye amene akudutsa mʼchipululu.* Dzina lake ndi Ya.*+ Sangalalani pamaso pake.
19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu kumwamba amene ankamveka ngati mawu ofuula a khamu lalikulu akuti: “Tamandani Ya!*+ Mulungu wathu amapulumutsa anthu ndipo ali ndi mphamvu zazikulu komanso ulemerero,