Salimo 25:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati munthu amaopa Yehova,+ Iye adzamulangiza njira imene akuyenera kusankha.+ נ [Nun] 13 Moyo wake udzasangalala ndi zinthu zabwino,+Ndipo mbadwa* zake zidzatenga dziko lapansi kuti likhale lawo.+ Salimo 37:25, 26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinali mwana ndipo tsopano ndakula,Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+ 26 Nthawi zonse amakongoza ena zinthu zake mokoma mtima,+Ndipo ana ake adzalandira madalitso.
12 Ngati munthu amaopa Yehova,+ Iye adzamulangiza njira imene akuyenera kusankha.+ נ [Nun] 13 Moyo wake udzasangalala ndi zinthu zabwino,+Ndipo mbadwa* zake zidzatenga dziko lapansi kuti likhale lawo.+
25 Ndinali mwana ndipo tsopano ndakula,Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+ 26 Nthawi zonse amakongoza ena zinthu zake mokoma mtima,+Ndipo ana ake adzalandira madalitso.