Deuteronomo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mʼdziko lanu mudzapitirizabe kupezeka anthu osauka.+ Nʼchifukwa chake ndikukulamulani kuti, ‘Muzikhala owolowa manja kwa mʼbale wanu wovutika komanso wosauka mʼdziko lanu.’+ Miyambo 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu amapereka mowolowa manja* ndipo pamapeto pake amakhala ndi zinthu zochuluka.+Munthu wina amaumira zimene amafunika kupatsa anthu ena, koma amasauka.+ Miyambo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amene amakomera mtima munthu wonyozeka akukongoza Yehova,+Ndipo adzamʼbwezera* zimene anachitazo.+
11 Mʼdziko lanu mudzapitirizabe kupezeka anthu osauka.+ Nʼchifukwa chake ndikukulamulani kuti, ‘Muzikhala owolowa manja kwa mʼbale wanu wovutika komanso wosauka mʼdziko lanu.’+
24 Munthu amapereka mowolowa manja* ndipo pamapeto pake amakhala ndi zinthu zochuluka.+Munthu wina amaumira zimene amafunika kupatsa anthu ena, koma amasauka.+
17 Amene amakomera mtima munthu wonyozeka akukongoza Yehova,+Ndipo adzamʼbwezera* zimene anachitazo.+