1 Samueli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Odya bwino ayenera kugwira ganyu kuti apeze chakudya,Koma anjala alibenso njala.+ Wosabereka wabereka ana 7,+Koma amene anali ndi ana aamuna ambiri, ali yekhayekha.* Yesaya 54:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 “Fuula mosangalala iwe mkazi amene sunaberekepo mwana.+ Iwe amene sunamvepo zowawa za pobereka,+ sangalala ndipo ufuule mosangalala.+Chifukwa ana a mkazi wosiyidwa ndi ambiriKuposa ana a mkazi yemwe ali ndi mwamuna,”*+ akutero Yehova.
5 Odya bwino ayenera kugwira ganyu kuti apeze chakudya,Koma anjala alibenso njala.+ Wosabereka wabereka ana 7,+Koma amene anali ndi ana aamuna ambiri, ali yekhayekha.*
54 “Fuula mosangalala iwe mkazi amene sunaberekepo mwana.+ Iwe amene sunamvepo zowawa za pobereka,+ sangalala ndipo ufuule mosangalala.+Chifukwa ana a mkazi wosiyidwa ndi ambiriKuposa ana a mkazi yemwe ali ndi mwamuna,”*+ akutero Yehova.