1 Mbiri 16:29, 30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mʼpatseni Yehova ulemerero woyenera dzina lake,+Bweretsani mphatso pamaso pake.+ Weramirani* Yehova mutavala zovala zokongola ndi zopatulika.+ 30 Dziko lonse lapansi linjenjemere pamaso pake! Dziko lapansi lakhazikika moti silingasunthidwe.*+
29 Mʼpatseni Yehova ulemerero woyenera dzina lake,+Bweretsani mphatso pamaso pake.+ Weramirani* Yehova mutavala zovala zokongola ndi zopatulika.+ 30 Dziko lonse lapansi linjenjemere pamaso pake! Dziko lapansi lakhazikika moti silingasunthidwe.*+