Habakuku 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi chifaniziro chosema chili ndi phindu lanji,Pamene munthu wachisema? Nanga chifaniziro chachitsulo ndi mphunzitsi wonama zili ndi phindu lanji,Ngakhale kuti wochipanga amachikhulupirira,Nʼkumapanga milungu yopanda pake yosalankhula?+
18 Kodi chifaniziro chosema chili ndi phindu lanji,Pamene munthu wachisema? Nanga chifaniziro chachitsulo ndi mphunzitsi wonama zili ndi phindu lanji,Ngakhale kuti wochipanga amachikhulupirira,Nʼkumapanga milungu yopanda pake yosalankhula?+