Salimo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa akufa satchula* za inu.Kodi ndi ndani amene angakutamandeni ali mʼManda?*+ Mlaliki 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse+ komanso salandira mphoto iliyonse,* chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zimaiwalika.+
5 Chifukwa amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse+ komanso salandira mphoto iliyonse,* chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zimaiwalika.+