Salimo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu wonyozekayu anaitana ndipo Yehova anamva. Anamupulumutsa ku mavuto ake onse.+ Aroma 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa “aliyense woitana pa dzina la Yehova* adzapulumuka.”+